John 6:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndidakuuzani kuti inde inu mwandiwona, komabe simukhulupirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinati kwa inu, kuti mungakhale mwandiona, simukhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga ndakuwuzani kale, ngakhale kuti mwandiona simukukhulupirirabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinati kwa inu, kuti mungakhale mwandiona, simukhulupirira.