John 6:50 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma chakudya chimene ndikunenachi ndi chimene chidatsika kuchokera Kumwamba, kuti munthu atachidya asafe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkate wotsika Kumwamba ndi uwu, kuti munthu akadyeko ndi kusamwalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pano pali chakudya chochokera kumwamba, chimene munthu akadya sangafe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
7 Mkate wotsika Kumwamba ndi uwu, kuti munthu akadyeko ndi kusamwalira.