John 6:60 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzira ambiri a Yesu atamva zimenezi adati, “Mau ameneŵa ngapatali. Angathe kuŵavomera ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ambiri a ophunzira ake, pakumva izi, anati, Mau awa ndi osautsa; akhoza kumva awa ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakumva izi ambiri a ophunzira ake anati, “Ichi ndi chiphunzitso chovuta. Angachilandire ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
14 Pamenepo ambiri a akuphunzira ace, pakumva izi, anati, Mau awa ndi osautsa; akhoza kumva awa ndani?