John 6:61 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adaadziŵa mumtima mwake kuti ophunzira ake akung'ung'udza za zimenezi. Tsono adaŵafunsa kuti, “Kodi zimenezi mukukhumudwa nazo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yesu podziwa mwa yekha kuti ophunzira ake alikung'ung'udza chifukwa cha ichi, anati kwa iwo, Ichi mukhumudwa nacho?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pozindikira kuti ophunzira ake ankangʼungʼudza, Yesu anawafunsa kuti, “Kodi izi zikukukhumudwitsani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yesu podziwa mwa yekha kuti akuphunzira ace alikung'ung'udza cifukwa ca ici, anati kwa iwo, ici mukhumudwa naco?