John 6:62 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga mudzatani mukadzaona Mwana wa Munthu akukwera kunka kumene anali kale?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga bwanji ngati mukaona Mwana wa Munthu alikukwera kumene anali kale lomwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga mutaona Mwana wa Munthu akukwera kupita kumene Iye anali poyamba!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
15 Nanga bwanji ngati mukaona Mwana wa munthu alikukwera kumene anali kale lomwe?