John 6:67 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yesu adafunsa ophunzira khumi ndi aŵiri aja kuti, “Nanga inu, kodi inunso mukufuna kuchoka?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yesu anati kwa khumi ndi awiriwo, Nanga inunso mufuna kuchoka?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anafunsa khumi ndi awiriwo kuti, “Kodi inu mukufuna kuchokanso?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yesu anati kwa khumi ndi awiriwo, Nanga inunso mufuna kucoka?