John 6:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pali mnyamata pano, ali ndi buledi msanu wabarele, ndi tinsomba tiŵiri. Koma zimenezi zingachitenji kwa anthu onseŵa?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pali mnyamata pano, amene ali nayo mikate isanu yabarele, ndi tinsomba tiwiri; koma nanga izi zifikira bwanji ambiri otere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pano pali mnyamata amene ali ndi buledi musanu wabarele ndi tinsomba tiwiri, kodi zingakwane onsewa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pali mnyamata pano, amene ali nayo mikate isanu yabarele, ndi tinsomba tiwiri; koma nanga izi zifikira bwanji ambiri otere?