John 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akulu a Ayuda ankamufunafuna kuchikondwereroko, nkumafunsana kuti, “Kodi amene uja ali kuti?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo Ayuda analikumfuna Iye pachikondwerero, nanena, Ali kuti uja?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano kuphwandoko Ayuda anakamufunafuna ndi kumafunsana kuti, “Kodi munthu ameneyu ali kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomwepo Ayuda analikumfuna iye paphwando, nanena, Ali kuti uja?