John 7:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe panalibe munthu wolankhula poyera za Iye, chifukwa choopa akulu a Ayuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana anatero panalibe munthu analankhula za Iye poyera, chifukwa cha kuopa Ayuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma panalibe amene ankanena kalikonse poyera za Iye chifukwa choopa Ayuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana anatero panalibe munthu analankhula za iye poyera, cifukwa ca kuopa Ayuda.