John 7:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma khamu la anthu lidamuyankha kuti, “Wagwidwa ndi mizimu yoipa Iwe. Akufuna kukupha ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khamu la anthu linayankha, Muli ndi chiwanda: afuna ndani kukuphani Inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu la anthu linayankha kuti, “Iwe ndiye wagwidwa ndi ziwanda. Ndani akufuna kukupha?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khamu la anthu linayankha, Muli ndi ciwanda: afuna ndani kukuphani lou?