John 7:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo anthu ena a ku Yerusalemu adati, “Kodi munthu akufuna kumupha uja, si ameneyu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyi anthu ena a ku Yerusalemu anayamba kufunsana kuti, “Kodi uyu si munthu uja akufuna kumuphayu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha r