John 7:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akunena kuti, ‘Mudzandifunafuna koma simudzandipeza,’ ndiponso kuti, ‘Kumene ndizikakhala Ine, inu simungakafikeko.’ Kodi mau ameneŵa akutanthauza chiyani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau awa amene ananena ndi chiyani, Mudzandifunafuna osandipeza Ine: ndipo pomwe ndili Ine, inu simungathe kudzapo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Iye amatanthauza chiyani pamene anati, ‘Inu mudzandifunafuna koma simudzandipeza,’ ndi ‘Kumene Ine ndili, inu simungathe kubwera?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau awa amene ananena ndi ciani, Mudzandifunafuna osandipeza Ine: ndipo pomwe ndiri Ine, inu simungathe kudzapo?