John 7:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene khamu la anthu lidamva mau ameneŵa, ena mwa iwo ankati, “Zoonadi munthuyu ndiye Mneneri uja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ena a khamulo pakumva mau awa, ananena, Mneneriyo ndi uyu ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakumva mawu ake, ena a anthuwo anati, “Zoonadi munthu uyu ndi mneneri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ena a khamulo pakumva mau awa, ananena, 2 Mnene riyo ndi uyu ndithu.