John 7:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena ankanena kuti, “Ameneyu ndiye Mpulumutsi wolonjezedwa uja.” Koma ena ankanena kuti, “Kodi Mpulumutsiyo nkuchokera ku Galileya ngati?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ena ananena, Uyu ndi Khristu. Koma ena ananena, Kodi Khristu adza kutuluka m'Galileya?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena anati, “Iye ndiye Khristu.” Komanso ena anafunsa kuti, “Kodi Khristu angachokere bwanji ku Galileya?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ena ananena, 3 Uyu ndi Kristu, Koma ena ananena, Kodi Kristu adza kuturuka m'Galileya?