John 7:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho khamu la anthu lidagaŵikana chifukwa cha Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudakhala tsono kusiyana m'khamulo chifukwa cha Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthu anagawikana chifukwa cha Yesu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
5 Kudakhala tsono kusiyana m'khamulo cifukwa ca iye.