John 7:48 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mudamvapo kuti pakati pa akuluakulu kapena pakati pa Afarisi alipo wokhulupirira amene uja?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi wina wa akulu anakhulupirira Iye, kapena wa Afarisi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi alipo ena a olamulira kapena a Afarisi, anamukhulupirira Iye?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
8 Kodi wina wa akuru anakhulupirira iye, kapena wa Afarisi?