John 7:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu wambaŵa sadziŵa Malamulo a Mose; ngotembereredwa basi!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma khamu ili losadziwa chilamulo, likhala lotembereredwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ayi! Koma gulu limene silidziwa malamulo ndi lotembereredwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma khamu ili losadziwa cilamulo, likhala lotembereredwa.