John 7:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Nikodemo, mmodzi mwa Afarisi, yemwe uja amene kale adaapita kwa Yesu, adafunsa anzakewo kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nikodemo ananena kwa iwo, amene uja adadza kwa Iye kale, ali mmodzi wa iwo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nekodimo, amene anapita kwa Yesu poyamba paja ndipo anali mmodzi wa iwo, anafunsa kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
9 Nikodemo ananena kwa iwo, amene uja adadza kwa iye kale, ali mmodzi wa iwo,