John 7:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adati, “Kani iwenso ndiwe wa ku Galileya? Kafunefune m'Malembo ndipo udzaona kuti palibe mneneri wochokera ku Galileya.” [
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayankha nati kwa iye, Kodi iwenso uli wotuluka m'Galileya? Santhula, nuone kuti m'Galileya sanauke mneneri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayankha kuti, “Kodi ndiwenso wochokera ku Galileya? Tayangʼananso, ndipo udzapeza kuti mneneri sachokera ku Galileya.” [Mipukutu yoyambirira ndi maumboni akale mulibe 7:53 mpaka 8:11]
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayankha nati kwa iye, Kodi iwenso uli woturuka m'Galileya? Santhula, nuone kuti m'Galileya sanauka mneneri.