John 8:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Afarisi adamuuza kuti, “Ukudzichitira wekha umboni. Umboni wakowo ngwosakwanira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Afarisi anati kwa Iye, Muchita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Afarisi anamutsutsa Iye nati, “Iwe ukudzichitira umboni wa Iwe mwini, umboni wako siwoona.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Afarisi anati kwa iye, Mucita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona.