John 8:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo m'Malamulo anu mudalembedwa kuti umboni wa anthu aŵiri ngwokwanira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde kudalembedwa m'chilamulo chanu kuti umboni wa anthu awiri uli woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalamulo anu munalembedwa kuti umboni wa anthu awiri ndi wovomerezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde kudalembedwa m'cilamulo canu kuti umboni wa anthu awiri uli woona.