John 8:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndimadzichitira ndekha umboni, nawonso Atate amene adandituma amandichitira umboni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndine wakuchita umboni wa Ine ndekha, ndipo Atate amene anandituma Ine achita umboni wa Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikudzichitira ndekha umboni; ndipo mboni inanso ndi Atate amene anandituma.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndine wakucita umboni wa Ine ndekha, ndipo Atate amene anandituma Ine, acita umboni wa Ine.