John 8:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mamaŵa adabweranso ku Nyumba ya Mulungu. Anthu onse adadza kwa Iye, Iyeyo nkukhala pansi nayamba kuŵaphunzitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mamawa anadzanso ku Kachisi, ndipo anthu onse anadza kwa Iye; ndipo m'mene anakhala pansi anawaphunzitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmamawa Iye anaonekeranso ku Nyumba ya Mulungu kumene anthu onse anamuzungulira ndipo Iye anakhala pansi nawaphunzitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komac mamawa anadzanso kuKacisi, ndipo anthu onse anadza kwa iye; ndipo m'mene anakhala pansi anawaphunzitsa.