John 8:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yesu adaŵauzanso kuti, “Ine ndikupita. Mudzandifunafuna koma mudzafera m'machimo anu. Kumene ndikupita Ine, inu simungathe kufikako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anatinso kwa iwo; Ndimuka Ine, ndipo mudzandifuna, ndipo m'tchimo lanu mudzafa: kumene ndimukako Ine, simudziwa kudza inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenakanso Yesu anawawuza kuti, “Ine ndikupita, ndipo mudzandifunafuna, koma mudzafa muli mʼmachimo anu. Kumene ndikupita, inu simungabwereko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anatinso kwa iwo; Ndimuka Ine, ndipo mudzandifuna, ndipo m'cimo lanu mudzafa: kumene ndimukako Ine, simudziwa kudza inu.