John 8:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu aja sadazindikire kuti Yesu akunena za Atate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanazindikira iwo kuti analikunena nao za Atate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo sanazindikire kuti Iye amawawuza za Atate ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanazindikira iwo kuti analikunena nao za Atate.