John 8:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapolo sakhala nao m'banja nthaŵi zonse, koma mwana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kapolo sakhala m'nyumba nthawi yonse; mwana ndiye akhala nthawi yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pajatu kapolo alibe malo wokhazikika mʼbanja, koma mwana ndi wa mʼbanjamo nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kapolo sakhala m'nyumba nthawi yonse; mwana ndiye akhala nthawi yonse.