John 8:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mukuchita zimene tate wanu amachita.” Iwo adamuuza kuti, “Ife ndiye sindife ana am'chigololotu ai. Tili ndi Tate mmodzi yekha, ndiye Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu muchita ntchito za atate wanu. Anati kwa Iye, Sitinabadwa ife m'chigololo; tili naye Atate mmodzi ndiye Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mukuchita zinthu zimene abambo anu amachita.” Iwo anatsutsa kuti, “Ife si ana amʼchigololo, Atate amene tili nawo ndi Mulungu yekha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mucita nchito za atate wanu. Anati kwa iye, Sitinabadwa ife m'cigololo; tiri naye Atate mmodzi ndiye Mulungu.