John 8:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga chifukwa chiyani simukumvetsa zimene ndikunena? Chifukwa chake nchakuti simungakonde konse kumva mau anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Simuzindikira malankhulidwe anga chifukwa ninji? Chifukwa simungathe kumva mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani simukumvetsetsa mawu anga? Chifukwa chake nʼchakuti simungathe kumva zoyankhula zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Simuzindikira malankhulidwe anga cifukwa ninji? Cifukwa simungathe kumva mau anga,