John 8:53 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga Iweyo nkupambana atate athu Abrahamu amene adamwalira? Anenerinso adamwalira. Kodi umadziyesa yani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Inu ndinu wamkulu ndi atate wathu Abrahamu, amene anamwalira? Ndipo aneneri anamwalira: mudziyesera nokha muli yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndinu wa mkulu kuposa abambo athu Abrahamu? Iye anafa, ndiponso aneneri onse. Inu mukuganiza kuti ndinu yani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Inu ndinu wamkulu ndi atate wathu Abrahamu, amene anamwalira? ndipo aneneri anamwalira: mudziyesera nokha muli yani?