John 9:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu ankayenda, adaona munthu wa khungu lobadwa nalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo popita, anaona munthu ali wosaona chibadwire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuyendabe, anaona munthu wosaona chibadwire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo popita, anaona munthu ali wosaona cibadwire.