John 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo anthu aja adamufunsa kuti, “Nanga maso ako apenya bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anenana ndi iye, Nanga maso ako anatseguka bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anafunsitsa kuti, “Kodi nanga maso ako anatsekuka bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananena ndi iye, Nanga maso ako anatseguka bwanji?