John 9:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adamufunsa kuti, “Kodi anachita chiyani pamene anakupenyetsa?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anati kwa iye, Anakuchitira iwe chiyani? Anakutsegulira iwe maso bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anamufunsa kuti, “Kodi Iye anachita chiyani kwa iwe? Iye anatsekula motani maso ako?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anati kwa iye, Anakucitira iweciani? anakutsegulira iwe maso bwanji?