John 9:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkale lomwe sikudamveke konse kuti wina adapenyetsa munthu wakhungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuyambira pachiyambi sikunamveka kuti wina anatsegulira maso munthu wosaona chibadwire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe amene anamvapo za kutsekula maso a munthu wobadwa wosaona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuyambira paciyambi sikunamveka kuti wina anatsegulira maso munthu wosaona cibadwire.