John 9:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu ameneyu akadapanda kuchokera kwa Mulungu, sakadatha konse kuchita kanthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati uyu sanachokera kwa Mulungu, sakadakhoza kuchita kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu uyu akanakhala wosachokera kwa Mulungu, palibe chimene Iye akanachita.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngatiuyu sanacokera kwa Mulungu, sakadakhoza kucita kanthu.