John 9:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndili pansi pano, ndine kuŵala kounikira anthu onse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakukhala Ine m'dziko lapansi, ndili kuunika kwa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Ine ndili mʼdziko lapansi, Ine ndine kuwunika kwa dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakukhala Ine m'dziko lapansi, ndiri kuunika kwa dziko lapansi.