Jonah 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adamufunsa kuti, “Kodi tikuchite chiyani kuti nyanjayi ikhale bata?” M'menemo nkuti namondwe uja akukulirakulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono anati kwa iye, Tichitenji nawe, kuti nyanja itichitire bata? Popeza namondwe anakulakulabe panyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Namondwe ananka nakulirakulirabe pa nyanjapo. Tsono anamufunsa iye kuti, “Kodi tikuchite chiyani kuti nyanjayi ikhale bata?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono anati kwa iye, Ticitenji nawe, kuti nyanja iticitire bata? popeza namondwe anakula-kulabe panyanja.