Jonah 1:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalinyero adayesetsa kupalasa kwambiri kuti abwerere ku mtunda, koma adalephera ndithu, poti mafunde ankakwererakwerera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma amunawo anapalasa kubwerera kumtunda, koma sanathe; pakuti namondwe wa panyanja anakulakula mokomana nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe oyendetsa sitimayo anayesetsa kupalasa kwambiri kuti abwerere ku mtunda koma analephera ndithu poti nyanja inawinduka kwambiri kuposa poyamba paja
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma amunawo anapalasa kubwerera kumtunda, koma sanathe; pakuti namondwe wa panyanja anakulakula mokomana nao.