Jonah 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adatama Chauta mopemba kuti, “Inu Chauta, takupembani musalole kuti ifeyo tife chifukwa cha moyo wa munthu uyu. Musatizenge mlandu chifukwa cha kupha munthu wosalakwa. Zonsezi zachitika chifukwa cha kufuna kwanu Inu Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anafuulira kwa Yehova, nati, Tikupemphanitu, Yehova, tisatayike chifukwa cha moyo wa munthu uyu, musatisenzetse mwazi wosachimwa; pakuti, Inu Yehova, mwachita monga mudakomera Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo iwo anafuwulira kwa Yehova nati, “Inu Yehova, musalole kuti ife tife chifukwa cha moyo wa munthu uyu. Musatizenge mlandu wa kupha munthu wosalakwa, pakuti ife tachita monga mwakufuna kwanu, Inu Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anapfuulira kwa Yehova, nati, Tikupemphanitu, Yehova, tisatayike cifukwa ca moyo wa munthu uyu, musatisenzetse mwazi wosacimwa; pakuti, Inu Yehova, mwacita monga mudakomera Inu.