Jonah 1:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adatuma chinsomba chachikulu kuti chimeze Yona. Motero Yonayo adakhala m'mimba mwa chinsombacho masiku atatu, usana ndi usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova anaikiratu chinsomba chachikulu chimeze Yona; ndipo Yona anali m'mimba mwa nsombayi masiku atatu usana ndi usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova anatuma nsomba yayikulu kuti imeze Yona. Motero Yona anakhala mʼmimba mwa nsombayo masiku atatu, usana ndi usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova anaikiratu cinsomba cacikuru cimeze Yona; ndipo Yona anali m'miroba mwa nsombayi masiku atatu usana ndi usiku.