Jonah 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nyamuka, upite ku Ninive, mzinda waukulu uja. Ukaŵadzudzule momveka ndithu anthu chifukwa ndaona kuipa kwao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyamuka, pita ku Ninive, mudzi waukuluwo, nulalikire motsutsana nao; pakuti choipa chao chandikwerera pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nyamuka, pita ku mzinda waukulu wa Ninive ndipo ukalalikire motsutsana nawo, chifukwa zoyipa zawo zafika pamaso panga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyamuka, pita ku Nineve, mudzi waukuruwo, nulalikire motsutsana nao; pakuti coipa cao candikwerera pamaso panga.