Jonah 1:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta adautsa namondwe, ndipo nyanja idayamba kuŵinduka kwambiri ndi namondweyo, kotero kuti chombo chinali pafupi kuwonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova anautsa chimphepo chachikulu panyanja, ndipo panali namondwe wamkulu panyanja, ndi chombo chikadasweka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova anatumiza chimphepo champhamvu pa nyanja, ndipo panauka namondwe wamphamvu amene anafuna kuphwanya sitimayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova anautsa cimphepo cacikuru panyanja, ndipo panali namondwe wamkuru panyanja, ndi combo cikadasweka.