Jonah 1:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono kaputeni wa chombo adafika kwa Yona uja namufunsa kuti, “Kodi iwe, nchiyani chimenechi? Monga iwe nkumagona eti? Dzuka, utame kwa Mulungu wako mopemba, mwina nkuwona watithandiza kuti tisamire.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwini chombo anadza kwa iye, nanena naye, Utani iwe wam'tulo? Uka, itana Mulungu wako, kapena Mulunguyo adzatikumbukira tingatayike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkulu wa oyendetsa sitimayo anapita kwa iye ndipo anati, “Kodi iwe, nʼchifukwa chiyani ukugona? Dzuka pemphera kwa mulungu wako! Mwina adzatithandiza, ndipo sitidzawonongeka.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwini combo anadza kwa iye, nanena naye, Utani iwe wam'tulo? uka, itana Mulungu wako, kapena Mulunguyo adzatikumbukila tingatayike.