Jonah 4:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma m'maŵa mwake mbandakucha, Mulungu adatuma mphanzi kuti ikadye msatsiwo, ndipo udafota.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Mulungu anauikira mphanzi pakucha m'mawa mwake, ndiyo inadya msatsi, nufota.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsiku linalo mmawa, Mulungu anabweretsa mbozi imene inadya msatsiyo ndipo inafota.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Mulungu anauikira mphanzi pakuca m'mawa mwace, ndiyo inadya msatsi, nufota.