Joshua 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Yoswa adauza fuko la Rubeni ndi la Gadi ndi theka la fuko la Manase kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anati kwa Arubeni, ndi Agadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yoswa anawuza fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi theka la fuko la Manase kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anati kwa Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, ndi kuti,