Joshua 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kumbukirani zija zimene Mose, mtumiki wa Chauta, adakuuzani, kuti, ‘Chauta, Mulungu wanu, adzakupatsani dziko limeneli kuti likhale lanu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kumbukirani zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani kuti, ‘Yehova Mulungu wanu akukupatsani mpumulo, ndi dziko ili kuti likhale lanu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.