Joshua 10:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chiyambire nkale lonse, sipadaonekepo tsiku longa limeneli loti Chauta adamvera munthu, popeza kuti ankamenyera Israele nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panalibe tsiku lotere kale lonse kapena m'tsogolomo, lakuti Yehova anamvera mau a munthu; pakuti Yehova anathirira Israele nkhondo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sipanakhaleponso tsiku ngati limeneli kuyambira kale, tsiku limene Yehova anamvera munthu. Izi zinatero chifukwa Yehova ankamenyera nkhondo Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panalibe tsiku lotere kale lonse kapena m'tsogolomo, lakuti Yehova anamvera mau a munthu; pakuti Yehova anathirira Israyeli nkhondo.