Joshua 10:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adapezeka, ndipo ena adadzauza Yoswa kuti mafumuwo akubisala kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauza Yoswa ndi kuti, Mafumu asanuwa apezeka obisala m'phanga la ku Makeda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yoswa anamva kuti mafumu asanu awapeza akubisala ku phanga la Makeda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauza Yoswa ndi kuti, Mafumu asanuwa apezeka obisala m'phanga la ku Makeda.