Joshua 10:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Yoswa pamodzi ndi Aisraele adapha anthuwo. Amene sadaphedwe ndi okhawo amene adabisala m'mizinda yamalinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, Yoswa ndi ana a Israele atatha kuwakantha, makanthidwe akulukulu mpaka atatha psiti, ndipo otsala a iwo atalowa m'midzi ya malinga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Yoswa ndi Aisraeli anapha anthu aja, kupatulapo ochepa amene anathawa nakabisala ku mizinda yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, Yoswa ndi ana a Israyeli atatha kuwakantha, makanthidwe akurukuru mpaka atatha psiti, ndipo otsala a iwo atalowa m'midzi ya malinga,