Joshua 10:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yoswa adapha mafumu onsewo naŵapachika pa mitengo isanu, ndipo adakhala pa mitengo imeneyo mpaka madzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatero, Yoswa anawakantha nawapha, nawapachika pa mitengo isanu; nalikupachikidwa pa mitengo mpaka madzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa anawabaya ndi kuwapha mafumuwo ndipo anawapachika pa mitengo isanu ndipo anakhala pamenepo mpaka madzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atatero, Yoswa anawakantha nawapha, nawapacika pa mitengo isanu; nalikupacikidwa pa mitengo mpaka madzulo.