Joshua 10:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yoswa pamodzi ndi Aisraele adapitirira kuchokera ku Makeda nakafika ku Libina, nauthira nkhondo mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yoswa ndi Aisraele onse naye anapitirira kuchokera ku Makeda kunka ku Libina, nathira nkhondo pa Libina;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa ndi Aisraeli onse anapitirira kuchokera ku Makeda nakafika ku Libina ndi kuthira nkhondo mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoswa ndi Aisrayeli onse naye anapitirira kucokera ku Makeda kumka ku Libina, nathira nkhondo pa Libina;